Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kudya kwake mudzadye motere, mudzakhale mutamangirira m’chiuno mwanu,+ mutavala nsapato+ ndiponso mutatenga ndodo m’dzanja lanu. Muzidzadya mofulumira. Ameneyu ndi pasika* wa Yehova.+

  • 2 Mafumu 4:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Nthawi yomweyo Elisa anauza Gehazi+ kuti: “Kokera chovala chako m’chiuno ndipo uchimange.+ Tenga ndodo yangayi+ uzipita. Ukakumana ndi munthu aliyense panjira usamupatse moni,+ ndipo munthu akakupatsa moni, usamuyankhe. Ukaike ndodo yangayi pankhope ya mwanayo.”+

  • 2 Mafumu 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mneneri Elisa anaitana mmodzi wa ana+ a aneneri n’kumuuza kuti: “Konzeka,*+ nyamula botolo ladothi+ la mafutali m’manja mwako, upite ku Ramoti-giliyadi.+

  • 1 Petulo 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Konzekeretsani maganizo anu kuti mugwire ntchito mwamphamvu,+ khalanibe oganiza bwino,+ ndipo ikani chiyembekezo chanu pa kukoma mtima kwakukulu+ kumene kudzafika kwa inu, Yesu Khristu akadzaonekera.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena