28 Chotero iye anapita ku nkhondo ndi Yehoramu mwana wa Ahabu kukamenyana ndi Hazaeli+ mfumu ya Siriya ku Ramoti-giliyadi.+ Koma Asiriyawo anakatha+ Yehoramu.
5 Anatsatira malangizo+ awo ndipo anapita kunkhondo ndi Yehoramu+ mwana wa Ahabu mfumu ya Isiraeli, kukamenyana ndi Hazaeli+ mfumu ya Siriya ku Ramoti-giliyadi.+ Kumeneko oponya mivi analasa Yehoramu.+