1 Mafumu 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno mfumu ya Isiraeli inauza atumiki ake kuti: “Kodi mukudziwa kuti mzinda wa Ramoti-giliyadi+ ndi wathu? Koma tikuzengereza kuulanda m’manja mwa mfumu ya Siriya.” 2 Mbiri 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako anafika kwa mfumu, ndipo mfumuyo inamufunsa kuti: “Mikaya, kodi tipite kukamenyana ndi Ramoti-giliyadi, kapena tisapite?” Nthawi yomweyo Mikaya anayankha kuti: “Pitani mukapambana. Iwo akaperekedwa m’manja mwanu.”+
3 Ndiyeno mfumu ya Isiraeli inauza atumiki ake kuti: “Kodi mukudziwa kuti mzinda wa Ramoti-giliyadi+ ndi wathu? Koma tikuzengereza kuulanda m’manja mwa mfumu ya Siriya.”
14 Kenako anafika kwa mfumu, ndipo mfumuyo inamufunsa kuti: “Mikaya, kodi tipite kukamenyana ndi Ramoti-giliyadi, kapena tisapite?” Nthawi yomweyo Mikaya anayankha kuti: “Pitani mukapambana. Iwo akaperekedwa m’manja mwanu.”+