2 Mafumu 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsiku lotsatira, Hazaeli anatenga chofunda n’kuchiviika m’madzi. Kenako anaphimba nacho mfumuyo kumaso+ moti inamwalira,+ ndipo Hazaeli+ anayamba kulamulira m’malo mwake. 2 Mafumu 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulanda dziko la Isiraeli pang’ono ndi pang’ono, ndipo Hazaeli+ anapitiriza kupha anthu m’madera onse a dziko la Isiraeli.
15 Tsiku lotsatira, Hazaeli anatenga chofunda n’kuchiviika m’madzi. Kenako anaphimba nacho mfumuyo kumaso+ moti inamwalira,+ ndipo Hazaeli+ anayamba kulamulira m’malo mwake.
32 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulanda dziko la Isiraeli pang’ono ndi pang’ono, ndipo Hazaeli+ anapitiriza kupha anthu m’madera onse a dziko la Isiraeli.