Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Zimiri anafika n’kukantha+ Ela mpaka kumupha, ndipo iye anayamba kulamulira m’malo mwake. Zimenezi zinachitika m’chaka cha 27 cha Asa mfumu ya Yuda.

  • 2 Mafumu 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano Ataliya,+ mayi wa Ahaziya+ ataona kuti mwana wake wafa, anapha ana onse achifumu.+

  • 2 Mafumu 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Salumu mwana wa Yabesi anam’chitira chiwembu+ Zekariya n’kumupha+ ku Ibuleamu,+ ndipo iye anayamba kulamulira m’malo mwake.

  • Yesaya 33:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Tsoka iwe amene ukulanda zinthu koma iweyo osalandidwa. Tsoka kwa iwe amene ukuchita zachinyengo pamene ena sanakuchitire zachinyengo.+ Ukadzangomaliza kulanda, nawenso udzalandidwa.+ Ukadzangomaliza kuchitira ena zachinyengo, iwonso adzakuchitira zachinyengo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena