2 Mbiri 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehoramu atayamba kulamulira mu ufumu wa bambo ake, iye analimbitsa ufumu wake. Chotero anapha abale ake+ onse ndi lupanga ndiponso akalonga ena a Isiraeli. Aroma 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 popeza anadzazidwa ndi zosalungama+ zonse, kuipa+ konse, kusirira konse kwa nsanje,+ ndi uchimo+ wonse. Mtima wawo unadzala kaduka,+ umbanda,+ ndewu,+ chinyengo+ ndi njiru.+ Anakonda manong’onong’o+
4 Yehoramu atayamba kulamulira mu ufumu wa bambo ake, iye analimbitsa ufumu wake. Chotero anapha abale ake+ onse ndi lupanga ndiponso akalonga ena a Isiraeli.
29 popeza anadzazidwa ndi zosalungama+ zonse, kuipa+ konse, kusirira konse kwa nsanje,+ ndi uchimo+ wonse. Mtima wawo unadzala kaduka,+ umbanda,+ ndewu,+ chinyengo+ ndi njiru.+ Anakonda manong’onong’o+