Maliko 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 zachigololo, kusirira kwa nsanje,+ kuchita zoipa, chinyengo, khalidwe lotayirira,+ diso la kaduka, mnyozo, kudzikweza, ndiponso kuchita zinthu mosaganizira ena.
22 zachigololo, kusirira kwa nsanje,+ kuchita zoipa, chinyengo, khalidwe lotayirira,+ diso la kaduka, mnyozo, kudzikweza, ndiponso kuchita zinthu mosaganizira ena.