Agalatiya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano, ntchito za thupi zimaonekera.+ Ntchitozi ndizo dama,*+ zinthu zodetsa, khalidwe lotayirira,+ Aefeso 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Popeza iwo tsopano sakuthanso kuzindikira makhalidwe abwino,+ anadzipereka okha ku khalidwe lotayirira+ kuti achite chonyansa+ chamtundu uliwonse mwadyera.+
19 Tsopano, ntchito za thupi zimaonekera.+ Ntchitozi ndizo dama,*+ zinthu zodetsa, khalidwe lotayirira,+
19 Popeza iwo tsopano sakuthanso kuzindikira makhalidwe abwino,+ anadzipereka okha ku khalidwe lotayirira+ kuti achite chonyansa+ chamtundu uliwonse mwadyera.+