1 Atesalonika 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti sitikukudandaulirani chifukwa cha maganizo olakwika kapena odetsedwa,+ kapenanso mwachinyengo ayi. 1 Petulo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero, lekani zoipa zonse,+ zachinyengo zonse, zachiphamaso, kaduka ndi mtundu uliwonse wa miseche.+
3 Pakuti sitikukudandaulirani chifukwa cha maganizo olakwika kapena odetsedwa,+ kapenanso mwachinyengo ayi.
2 Chotero, lekani zoipa zonse,+ zachinyengo zonse, zachiphamaso, kaduka ndi mtundu uliwonse wa miseche.+