Yesaya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sambani,+ dziyeretseni.+ Chotsani zochita zanu zoipa pamaso panga.+ Lekani kuchita zoipa.+ Agalatiya 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’malomwake ndikuti, Pitirizani kuyenda mwa mzimu,+ ndipo simudzatsatira chilakolako cha thupi ngakhale pang’ono.+ Yakobo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho siyani khalidwe lililonse lonyansa ndiponso siyani khalidwe lochita zoipa, lomwe ndi losafunika,+ ndipo vomerezani mofatsa mawu okhoza kupulumutsa miyoyo yanu,+ kuti abzalidwe mwa inu.+
16 M’malomwake ndikuti, Pitirizani kuyenda mwa mzimu,+ ndipo simudzatsatira chilakolako cha thupi ngakhale pang’ono.+
21 Choncho siyani khalidwe lililonse lonyansa ndiponso siyani khalidwe lochita zoipa, lomwe ndi losafunika,+ ndipo vomerezani mofatsa mawu okhoza kupulumutsa miyoyo yanu,+ kuti abzalidwe mwa inu.+