Agalatiya 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 kaduka, kumwa mwauchidakwa,*+ maphwando aphokoso, ndi zina zotero. Ponena za zinthu zimenezi, ndikukuchenjezeranitu, ngati mmene ndinachitira poyamba paja, kuti anthu amene amachita zimenezi+ sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.+ Aefeso 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 kuti muvule umunthu wakale+ umene umagwirizana ndi khalidwe lanu lakale, umenenso ukuipitsidwa+ malinga ndi zilakolako zonyenga za umunthuwo.+
21 kaduka, kumwa mwauchidakwa,*+ maphwando aphokoso, ndi zina zotero. Ponena za zinthu zimenezi, ndikukuchenjezeranitu, ngati mmene ndinachitira poyamba paja, kuti anthu amene amachita zimenezi+ sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.+
22 kuti muvule umunthu wakale+ umene umagwirizana ndi khalidwe lanu lakale, umenenso ukuipitsidwa+ malinga ndi zilakolako zonyenga za umunthuwo.+