Nahumu 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense wokuona adzakuthawa+ ndipo adzanena kuti, ‘Nineve wasakazidwa! Ndani adzamuchitira chisoni?’ Kodi anthu oti akutonthoze ndiwapeza kuti?
7 Aliyense wokuona adzakuthawa+ ndipo adzanena kuti, ‘Nineve wasakazidwa! Ndani adzamuchitira chisoni?’ Kodi anthu oti akutonthoze ndiwapeza kuti?