Nahumu 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuchokera pamene Nineve anakhalapo,+ iye wakhala ngati dziwe la madzi,+ koma tsopano anthu ake akuthawa. Ena akufuula kuti: “Imani amuna inu! Imani!” Koma palibe amene akubwerera.+
8 Kuchokera pamene Nineve anakhalapo,+ iye wakhala ngati dziwe la madzi,+ koma tsopano anthu ake akuthawa. Ena akufuula kuti: “Imani amuna inu! Imani!” Koma palibe amene akubwerera.+