13 M’chaka cha 14 cha Mfumu Hezekiya, Senakeribu+ mfumu ya Asuri+ anabwera kudzachita nkhondo ndi mizinda yonse ya Ayuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, ndipo analanda mizindayo.
21 Ahazi anatenga zinthu za m’nyumba ya Yehova,+ za m’nyumba ya mfumu+ ndi za m’nyumba za akalonga,+ n’kuzipereka kwa mfumu ya Asuri+ monga mphatso, koma zimenezi sizinam’thandize.