Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 17:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye ndiye amene Salimanesere+ mfumu ya Asuri+ anabwera kudzamuthira nkhondo. Chotero Hoshiya anakhala mtumiki wake n’kuyamba kupereka msonkho+ kwa iye.

  • Yesaya 8:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 popeza mwanayo asanadziwe kuitana+ kuti, ‘Ababa!’ kapena ‘Amama!’ anthu adzanyamula chuma cha ku Damasiko ndi katundu wolandidwa ku Samariya n’kupita naye pamaso pa mfumu ya Asuri.”+

  • Yesaya 10:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Chotero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ wanena kuti: “Anthu anga amene mukukhala m’Ziyoni,+ musachite mantha chifukwa cha Msuri amene anali kukukwapulani ndi chikwapu+ ndiponso kukumenyani ndi ndodo, ngati mmene Iguputo anali kuchitira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena