Yesaya 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mwanayo asanafike podziwa kukana choipa ndi kusankha chabwino,+ nthaka ya mafumu awiri amene ukuchita nawo mantha ofika podwala nawowo, idzakhala itasiyidwiratu.+
16 Mwanayo asanafike podziwa kukana choipa ndi kusankha chabwino,+ nthaka ya mafumu awiri amene ukuchita nawo mantha ofika podwala nawowo, idzakhala itasiyidwiratu.+