Machitidwe 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu+ mokweza mawu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa,+ Inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zokhala mmenemo.+ Aheberi 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 pamsonkhano wawo waukulu.+ Kumenenso kuli mpingo wa woyamba kubadwayo,+ mpingo wa iwo amene analembedwa+ kumwamba. Kumeneko kulinso Mulungu, Woweruza wa onse,+ ndiponso kuli moyo wauzimu wa olungama+ amene akhala angwiro.+
24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu+ mokweza mawu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa,+ Inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zokhala mmenemo.+
23 pamsonkhano wawo waukulu.+ Kumenenso kuli mpingo wa woyamba kubadwayo,+ mpingo wa iwo amene analembedwa+ kumwamba. Kumeneko kulinso Mulungu, Woweruza wa onse,+ ndiponso kuli moyo wauzimu wa olungama+ amene akhala angwiro.+