2 Mbiri 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero Sisaki+ mfumu ya Iguputo anaukira Yerusalemu ndi kutenga chuma cha m’nyumba ya Yehova+ ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Anatenga chilichonse kuphatikizapo zishango zagolide zimene Solomo anapanga.+
9 Chotero Sisaki+ mfumu ya Iguputo anaukira Yerusalemu ndi kutenga chuma cha m’nyumba ya Yehova+ ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Anatenga chilichonse kuphatikizapo zishango zagolide zimene Solomo anapanga.+