26 Iye anatenga chuma cha m’nyumba ya Yehova ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Anatenga chilichonse+ kuphatikizapo zishango zonse zagolide zimene Solomo anapanga.+
14 Yehoasi anatenga golide ndi siliva yense, ndi ziwiya zonse zimene anazipeza panyumba ya Yehova+ ndi m’nyumba yosungiramo chuma cha mfumu. Anagwiranso anthu ena n’kubwerera ku Samariya.