2 Mbiri 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero Sisaki+ mfumu ya Iguputo anaukira Yerusalemu ndi kutenga chuma cha m’nyumba ya Yehova+ ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Anatenga chilichonse kuphatikizapo zishango zagolide zimene Solomo anapanga.+ Salimo 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zoonadi, munthu amayenda ngati chithunzithunzi.+Ndithudi, anthu amapokosera pachabe.+Munthu amaunjika zinthu ndipo sadziwa amene adzazitute.+
9 Chotero Sisaki+ mfumu ya Iguputo anaukira Yerusalemu ndi kutenga chuma cha m’nyumba ya Yehova+ ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Anatenga chilichonse kuphatikizapo zishango zagolide zimene Solomo anapanga.+
6 Zoonadi, munthu amayenda ngati chithunzithunzi.+Ndithudi, anthu amapokosera pachabe.+Munthu amaunjika zinthu ndipo sadziwa amene adzazitute.+