1 Mafumu 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inapanganso zishango 300 zing’onozing’ono za golide wosakaniza ndi zitsulo zina. (Chishango chaching’ono chilichonse anachikuta ndi golide wolemera ma mina* atatu.)+ Kenako mfumuyo inaika zishangozi m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni.+ 2 Mbiri 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumu Solomo inapanga zishango 200 zikuluzikulu zagolide wosakaniza ndi zitsulo zina.+ (Chishango chachikulu chilichonse anachikuta ndi golide wosakaniza ndi zitsulo zina wolemera masekeli 600.)+
17 Inapanganso zishango 300 zing’onozing’ono za golide wosakaniza ndi zitsulo zina. (Chishango chaching’ono chilichonse anachikuta ndi golide wolemera ma mina* atatu.)+ Kenako mfumuyo inaika zishangozi m’nyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni.+
15 Mfumu Solomo inapanga zishango 200 zikuluzikulu zagolide wosakaniza ndi zitsulo zina.+ (Chishango chachikulu chilichonse anachikuta ndi golide wosakaniza ndi zitsulo zina wolemera masekeli 600.)+