Numeri 35:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo ngati chifukwa chodana naye anamukankha,+ kapena ngati anamulasa ndi chinthu atamubisalira,+ mnzakeyo n’kufa, Deuteronomo 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Koma pakakhala munthu wodana+ ndi mnzake amene wabisalira ndi kuukira mnzakeyo panjira n’kumukantha ndipo wafa,+ iye n’kuthawira ku umodzi mwa mizinda imeneyi,
20 Ndipo ngati chifukwa chodana naye anamukankha,+ kapena ngati anamulasa ndi chinthu atamubisalira,+ mnzakeyo n’kufa,
11 “Koma pakakhala munthu wodana+ ndi mnzake amene wabisalira ndi kuukira mnzakeyo panjira n’kumukantha ndipo wafa,+ iye n’kuthawira ku umodzi mwa mizinda imeneyi,