Ekisodo 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Amene wamenya munthu mpaka munthuyo kufa ayenera kuphedwa ndithu.+ Numeri 35:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ngati munthu wamenya mnzake ndi chitsulo, mnzakeyo n’kufa, ameneyo ndi wakupha munthu.+ Ndipo wakupha munthuyo ayenera kuphedwa ndithu.+ Deuteronomo 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “‘Wotembereredwa ndi munthu wobisalira mnzake ndi kumupha.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
16 “‘Ngati munthu wamenya mnzake ndi chitsulo, mnzakeyo n’kufa, ameneyo ndi wakupha munthu.+ Ndipo wakupha munthuyo ayenera kuphedwa ndithu.+
24 “‘Wotembereredwa ndi munthu wobisalira mnzake ndi kumupha.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)