Numeri 35:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ngati munthu wamenya mnzake ndi chitsulo nʼkufa, ameneyo ndi wopha munthu. Ndipo wopha munthuyo ayenera kuphedwa ndithu.+
16 Koma ngati munthu wamenya mnzake ndi chitsulo nʼkufa, ameneyo ndi wopha munthu. Ndipo wopha munthuyo ayenera kuphedwa ndithu.+