Numeri 35:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ngati munthu wamenya mnzake ndi chitsulo, mnzakeyo n’kufa, ameneyo ndi wakupha munthu.+ Ndipo wakupha munthuyo ayenera kuphedwa ndithu.+
16 “‘Ngati munthu wamenya mnzake ndi chitsulo, mnzakeyo n’kufa, ameneyo ndi wakupha munthu.+ Ndipo wakupha munthuyo ayenera kuphedwa ndithu.+