Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 21:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Munthu amene wapsera mtima mnzake mpaka kumupha mwachiwembu,+ ngakhale atathawira kuguwa langa lansembe kuti atetezeke, muzimuchotsa n’kukamupha.+

  • Deuteronomo 19:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Koma pakakhala munthu wodana+ ndi mnzake amene wabisalira ndi kuukira mnzakeyo panjira n’kumukantha ndipo wafa,+ iye n’kuthawira ku umodzi mwa mizinda imeneyi,

  • Salimo 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iye amabisalira anthu pafupi ndi midzi.

      Amabisalira munthu wosalakwa ndi kumupha.+

      ע [ʽAʹyin]

      Maso ake amafunafuna waumphawi.+

  • Miyambo 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chotero anthu ochimwa amabisala kuti akhetse magazi a anthu ena.+ Amabisalira miyoyo ya anthu ena.+

  • Maliko 6:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Choncho Herodiya anam’sungira chidani mumtima+ ndipo anali kufuna kumupha, koma sanathe kutero.+

  • Machitidwe 23:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma chonde musalole kuti akunyengerereni, pakuti amuna oposa 40 akumudikirira panjira.+ Amenewa achita kulumbira modzitemberera kuti sadya kapena kumwa kanthu kufikira atamupha.+ Moti panopa akonzeka, akungoyembekezera chilolezo chanu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena