11 “Koma pakakhala munthu wodana+ ndi mnzake amene wabisalira ndi kuukira mnzakeyo panjira n’kumukantha ndipo wafa,+ iye n’kuthawira ku umodzi mwa mizinda imeneyi,
27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anam’tengera pambali kuchipata kuti alankhulane naye pa awiri.+ Koma kumeneko anamubaya pamimba+ moti anafa chifukwa chokhetsa magazi a Asaheli,+ m’bale wake wa Yowabu.