Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 21:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Munthu amene wapsera mtima mnzake mpaka kumupha mwachiwembu,+ ngakhale atathawira kuguwa langa lansembe kuti atetezeke, muzimuchotsa n’kukamupha.+

  • Deuteronomo 1:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Motero ine ndinalankhula nanu, ndipo simunamvere koma munayamba kupandukira+ lamulo la Yehova ndi kuchita zinthu modzikuza, motero munanyamuka kupita m’phiri.+

  • Deuteronomo 17:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munthu amene adzadzikuza mwa kusamvera wansembe amene akutumikira Yehova Mulungu wako kapena mwa kusamvera woweruza,+ munthu ameneyo afe ndithu.+ Muzichotsa woipayo mu Isiraeli.+

  • Aheberi 10:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pakuti ngati tikuchita machimo mwadala+ pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibe nsembe ina yotsala imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena