Salimo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso mundiletse kuchita modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+Pamenepo ndidzakhala wopanda chifukwa,+Ndipo ndidzakhalabe wopanda milandu yambiri yophwanya malamulo. Miyambo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+ Hoseya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Komabe, munthu asatsutse+ kapena kudzudzula anthu amenewa, chifukwa anthu a mtundu wako ali ngati munthu wotsutsana ndi wansembe.+
13 Komanso mundiletse kuchita modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+Pamenepo ndidzakhala wopanda chifukwa,+Ndipo ndidzakhalabe wopanda milandu yambiri yophwanya malamulo.
2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+
4 “Komabe, munthu asatsutse+ kapena kudzudzula anthu amenewa, chifukwa anthu a mtundu wako ali ngati munthu wotsutsana ndi wansembe.+