2 Samueli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno pambuyo pake, Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndipite ku umodzi mwa mizinda ya Yuda?” Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Pita.” Davide anafunsanso kuti: “Ndipite kuti?” Iye anamuyankha kuti: “Ku Heburoni.”+ 2 Samueli 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Abineri atafika kwa Davide ku Heburoni pamodzi ndi amuna 20, Davide anakonzera phwando+ Abineri ndi amuna amene anali naye.
2 Ndiyeno pambuyo pake, Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndipite ku umodzi mwa mizinda ya Yuda?” Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Pita.” Davide anafunsanso kuti: “Ndipite kuti?” Iye anamuyankha kuti: “Ku Heburoni.”+
20 Abineri atafika kwa Davide ku Heburoni pamodzi ndi amuna 20, Davide anakonzera phwando+ Abineri ndi amuna amene anali naye.