Levitiko 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako mnyamatayo anayamba kunyoza ndi kutukwana+ dzina la Mulungu.+ Chotero anabwera naye kwa Mose.+ Dzina la mayi ake linali Selomiti, mwana wa Dibiri, wa fuko la Dani. Yesaya 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
11 Kenako mnyamatayo anayamba kunyoza ndi kutukwana+ dzina la Mulungu.+ Chotero anabwera naye kwa Mose.+ Dzina la mayi ake linali Selomiti, mwana wa Dibiri, wa fuko la Dani.
23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+