21 Aliyense adzadutsa m’dzikolo akuzunzika ndiponso ali ndi njala.+ Chifukwa chakuti ali ndi njala ndiponso wakwiya, adzatukwana mfumu yake ndi Mulungu+ wake ndipo azidzayang’ana kumwamba.
9 Choncho anthu anapsa ndi kutentha kwakukulu. Koma iwo ananyoza dzina la Mulungu,+ amene ali ndi ulamuliro+ pa miliri imeneyi, ndipo sanalape kuti amupatse ulemerero.+