Deuteronomo 28:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+ 2 Mafumu 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala+ inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+ Yeremiya 52:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+ Maliro 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Lilime la ana oyamwa lamamatira kummero chifukwa cha ludzu.+Ana apempha chakudya+ koma palibe amene akuwapatsa.+
48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+
3 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala+ inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+
6 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+
4 Lilime la ana oyamwa lamamatira kummero chifukwa cha ludzu.+Ana apempha chakudya+ koma palibe amene akuwapatsa.+