2 Mafumu 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala+ inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+ Yeremiya 39:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’chaka cha 11 cha ulamuliro wa Zedekiya, m’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9, anaboola mpanda wa mzindawo.+
3 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala+ inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+
2 M’chaka cha 11 cha ulamuliro wa Zedekiya, m’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9, anaboola mpanda wa mzindawo.+