Maliro 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu ake onse akuusa moyo. Iwo akufunafuna chakudya.+Asinthanitsa zinthu zawo zabwino ndi chakudya kuti adzitsitsimutse.+Inu Yehova ndiyang’aneni. Onani kuti ndakhala ngati mkazi wachabechabe.+ Maliro 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anali kufunsa amayi awo kuti: “Kodi chakudya ndi vinyo zili kuti?”+Anali kufunsa chifukwa anali kukomoka m’mabwalo a mzinda ndi kugona pansi ngati anthu ophedwa,Ndiponso chifukwa moyo wawo unali kukhuthukira pachifuwa cha amayi awo.
11 Anthu ake onse akuusa moyo. Iwo akufunafuna chakudya.+Asinthanitsa zinthu zawo zabwino ndi chakudya kuti adzitsitsimutse.+Inu Yehova ndiyang’aneni. Onani kuti ndakhala ngati mkazi wachabechabe.+
12 Iwo anali kufunsa amayi awo kuti: “Kodi chakudya ndi vinyo zili kuti?”+Anali kufunsa chifukwa anali kukomoka m’mabwalo a mzinda ndi kugona pansi ngati anthu ophedwa,Ndiponso chifukwa moyo wawo unali kukhuthukira pachifuwa cha amayi awo.