Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 38:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Inu mbuyanga mfumu, zimene anthu awa achitira mneneri Yeremiya ndi zoipa, chifukwa amuponya m’chitsime, ndipo afera momwemo+ chifukwa cha njala,+ pakuti mkate watheratu mumzindawu.”

  • Yeremiya 52:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+

  • Maliro 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iwo anali kufunsa amayi awo kuti: “Kodi chakudya ndi vinyo zili kuti?”+

      Anali kufunsa chifukwa anali kukomoka m’mabwalo a mzinda ndi kugona pansi ngati anthu ophedwa,

      Ndiponso chifukwa moyo wawo unali kukhuthukira pachifuwa cha amayi awo.

  • Maliro 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Lilime la ana oyamwa lamamatira kummero chifukwa cha ludzu.+

      Ana apempha chakudya+ koma palibe amene akuwapatsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena