Yeremiya 38:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Inu mbuyanga mfumu, zimene anthu awa achitira mneneri Yeremiya ndi zoipa. Iwo amuponya mʼchitsime ndipo afera momwemo chifukwa cha njala, popeza mkate watheratu mumzindawu.”+
9 “Inu mbuyanga mfumu, zimene anthu awa achitira mneneri Yeremiya ndi zoipa. Iwo amuponya mʼchitsime ndipo afera momwemo chifukwa cha njala, popeza mkate watheratu mumzindawu.”+