Yeremiya 38:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Inu mbuyanga mfumu, zimene anthu awa achitira mneneri Yeremiya ndi zoipa, chifukwa amuponya m’chitsime, ndipo afera momwemo+ chifukwa cha njala,+ pakuti mkate watheratu mumzindawu.”
9 “Inu mbuyanga mfumu, zimene anthu awa achitira mneneri Yeremiya ndi zoipa, chifukwa amuponya m’chitsime, ndipo afera momwemo+ chifukwa cha njala,+ pakuti mkate watheratu mumzindawu.”