Genesis 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Popeza mwadzera njira yodutsa kwa kapolo wanu, mundilole ndikukonzereni kachakudya kuti mutsitsimutse mitima yanu.+ Mukatero mukhoza kupitiriza ulendo wanu.” Pamenepo iwo anati: “Chabwino, chita mmene waneneramo.” Nyimbo ya Solomo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu inu ndipatseni mphesa zouma zoumba pamodzi kuti zinditsitsimule.+ Ndipatseni maapozi kuti ndisafe chifukwa chikondi chikundidwalitsa.+
5 Popeza mwadzera njira yodutsa kwa kapolo wanu, mundilole ndikukonzereni kachakudya kuti mutsitsimutse mitima yanu.+ Mukatero mukhoza kupitiriza ulendo wanu.” Pamenepo iwo anati: “Chabwino, chita mmene waneneramo.”
5 Anthu inu ndipatseni mphesa zouma zoumba pamodzi kuti zinditsitsimule.+ Ndipatseni maapozi kuti ndisafe chifukwa chikondi chikundidwalitsa.+