19 Kuwonjezera apo, anthu onse, khamu lonse la Isiraeli, mwamuna komanso mkazi, aliyense wa iwo anapatsidwa+ keke yozungulira yoboola pakati, zipatso za kanjedza zouma zoumba pamodzi ndi mphesa zouma zoumba pamodzi.+ Kenako aliyense wa anthuwo anapita kunyumba yake.