Nyimbo ya Solomo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipatseni mphesa zouma zoumba pamodzi+ kuti zinditsitsimule.Ndipatseni maapozi kuti ndipeze mphamvu,Chifukwa chikondi chikundidwalitsa.
5 Ndipatseni mphesa zouma zoumba pamodzi+ kuti zinditsitsimule.Ndipatseni maapozi kuti ndipeze mphamvu,Chifukwa chikondi chikundidwalitsa.