1 Samueli 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli anali kukonda Davide, ndipo anthu anauza Sauli zimenezi. Sauli atamva nkhani imeneyi anasangalala. Nyimbo ya Solomo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ndakulumbiritsani+ inu ana aakazi a ku Yerusalemu+ kuti mukam’peza wachikondi wanga,+ mumuuze kuti ine chikondi chikundidwalitsa.”+
20 Tsopano Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli anali kukonda Davide, ndipo anthu anauza Sauli zimenezi. Sauli atamva nkhani imeneyi anasangalala.
8 “Ndakulumbiritsani+ inu ana aakazi a ku Yerusalemu+ kuti mukam’peza wachikondi wanga,+ mumuuze kuti ine chikondi chikundidwalitsa.”+