Nyimbo ya Solomo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu inu ndipatseni mphesa zouma zoumba pamodzi kuti zinditsitsimule.+ Ndipatseni maapozi kuti ndisafe chifukwa chikondi chikundidwalitsa.+
5 Anthu inu ndipatseni mphesa zouma zoumba pamodzi kuti zinditsitsimule.+ Ndipatseni maapozi kuti ndisafe chifukwa chikondi chikundidwalitsa.+