Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 24:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Munthu wotemberera dzina la Mulungu uja, mum’tulutsire kunja kwa msasa.+ Onse amene anamumva aike manja awo+ pamutu pake ndipo khamu lonse lim’ponye miyala.+

  • Yohane 10:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 nanga kodi inu mukundiuza ine woyeretsedwa ndi Atate ndi kutumizidwa m’dziko kuti, ‘Ukunyoza Mulungu,’ chifukwa ndanena kuti, Ndine Mwana wa Mulungu?+

  • Yuda 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 kudzapereka chiweruzo kwa onse,+ ndi kudzagamula kuti onse osaopa Mulungu apezeka ndi mlandu chifukwa cha ntchito zawo zonyoza Mulungu zimene anazichita mosaopa Mulungu, komanso chifukwa cha zinthu zonse zonyoza koopsa zimene ochimwa osaopa Mulungu anamunenera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena