Malaki 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Inu mwandinenera mawu achipongwe,”+ watero Yehova. Koma mukunena kuti: “Ife takunenerani zachipongwe zotani?”+ Mateyu 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndikukuuzani kuti pa Tsiku la Chiweruzo, anthu adzayankha mlandu pa mawu alionse opanda pake amene iwo amalankhula.+
13 “Inu mwandinenera mawu achipongwe,”+ watero Yehova. Koma mukunena kuti: “Ife takunenerani zachipongwe zotani?”+
36 Ndikukuuzani kuti pa Tsiku la Chiweruzo, anthu adzayankha mlandu pa mawu alionse opanda pake amene iwo amalankhula.+