Levitiko 13:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Masiku onse pamene akudwala nthendayo azikhala wodetsedwa. Iye ndi wodetsedwa ndipo azikhala payekha. Azikhala kunja kwa msasa.+ Numeri 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kaya akhale mwamuna kapena mkazi, uziwatulutsa kunja kwa msasa+ kuti asadetse+ misasa ya anthu amene ine ndikukhala pakati pawo.”+
46 Masiku onse pamene akudwala nthendayo azikhala wodetsedwa. Iye ndi wodetsedwa ndipo azikhala payekha. Azikhala kunja kwa msasa.+
3 Kaya akhale mwamuna kapena mkazi, uziwatulutsa kunja kwa msasa+ kuti asadetse+ misasa ya anthu amene ine ndikukhala pakati pawo.”+