Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndipo mundipangire malo opatulika, popeza ndiyenera kukhala pakati panu.+

  • Levitiko 26:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ine ndidzaika chihema changa chopatulika pakati panu,+ ndipo sindidzanyansidwa nanu.+

  • Yoswa 22:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ngati n’zoona kuti dziko lanu n’lodetsedwa,+ wolokerani kudziko la Yehova+ kumene kuli chihema chopatulika cha Yehova,+ mukakhazikike pakati pathu. Koma musapandukire Yehova, ndipo musachititse ifeyo kupanduka chifukwa cha guwa lansembe limene mwamangali, kuwonjezera pa guwa lansembe la Yehova Mulungu wathu.+

  • 2 Akorinto 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndipo pali kumvana kotani pakati pa kachisi wa Mulungu ndi mafano?+ Pakuti ifeyo ndife kachisi+ wa Mulungu wamoyo, monga ananenera Mulungu kuti: “Ndidzakhala pakati pawo+ ndi kuyenda pakati pawo. Ndidzakhala Mulungu wawo, ndipo iwo adzakhala anthu anga.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena