Levitiko 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo musatsatire mfundo za mitundu imene ndikuichotsa pamaso panu,+ chifukwa iwo amachita zonsezi ndipo amandinyansa.+ Yeremiya 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma chifukwa cha dzina lanu, musatisiye.+ Musanyazitse mpando wanu wachifumu waulemerero.+ Kumbukirani pangano lanu limene munachita ndi ife ndipo musaliphwanye.+
23 Ndipo musatsatire mfundo za mitundu imene ndikuichotsa pamaso panu,+ chifukwa iwo amachita zonsezi ndipo amandinyansa.+
21 Koma chifukwa cha dzina lanu, musatisiye.+ Musanyazitse mpando wanu wachifumu waulemerero.+ Kumbukirani pangano lanu limene munachita ndi ife ndipo musaliphwanye.+