13 Kumbukirani Abulahamu, Isaki ndi Isiraeli atumiki anu, amene munawalumbirira pa inu mwini,+ powauza kuti, ‘Ndidzachulukitsa mbewu yanu ngati nyenyezi zakumwamba,+ ndipo dziko lonseli limene ndalipatula ndidzalipereka kwa mbewu yanu,+ kuti likhale lawo mpaka kalekale.’”+