Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 17:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Ndidzakwaniritsa pangano langa la pakati pa ine ndi iwe,+ ndi mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe ku mibadwomibadwo. Lidzakhala pangano mpaka kalekale,+ kusonyeza kuti ndine Mulungu wako ndi wa mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe.+

  • Levitiko 26:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Chotero ndidzakumbukira pangano langa limene ndinachita ndi Yakobo.+ Ndidzakumbukiranso pangano langa ndi Isaki+ komanso ndi Abulahamu.+ Ndidzakumbukiranso dzikolo.

  • Deuteronomo 4:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wachifundo.+ Sadzakutayani kapena kukuwonongani kapena kuiwala pangano+ la makolo anu limene anawalumbirira.

  • Deuteronomo 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Ndiyeno mukapitiriza kumvera zigamulo zimenezi ndi kuzisunga,+ Yehova Mulungu wanu adzasunga pangano+ ndi kukusonyezani kukoma mtima kosatha, zimene analumbirira makolo anu.+

  • Salimo 105:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Wakumbukira pangano lake mpaka kalekale,+

      Wakumbukira lonjezo limene anapereka ku mibadwo 1,000,+

  • Salimo 106:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+

      Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena